2 Mbiri 26:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uziya anali wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi asanu mphambu ziwiri; ndi dzina la mace ndiye Yekoliya wa ku Yerusalemu.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:1-13