2 Mbiri 26:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Azariya wansembe wamkulu, ndi ansembe onse, anampenya, ndi kuona kuti anali wakhate pamphumi pace namkankhiza msanga kubwalo; nafulumiranso yekha kuturukako, pakuti Yehova adamkantha.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:10-22