2 Mbiri 26:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Azariya wansembe analowa pambuyo pace, ndi pamodzi naye ansembe a Yehova makumi asanu ndi atatu, ndiwo olimba mtima;

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:10-22