2 Mbiri 26:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Napanga m'Yerusalemu makina, opangidwa ndi eni luso, akhale pansanja ndi kungondya, aponye nao mibvi ndi miyala yaikuru. Ndi dzina lace linamveka kutali; pakuti anathandizidwa modabwiza, mpaka analimbikatu.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:7-20