2 Mbiri 26:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'dzanja mwao munali khamu la nkhondo zikwi mazana atatu mphambu zikwi zisanu ndi ziwiri kudza mazana asanu ocita nkhondo ndi mphamvu yaikuru, kuthandiza mfumu alimbane ndi adani.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:10-14