2 Mbiri 26:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Uziya anali nalonso khamu la anthu a nkhondo, oturuka kunkhondo magulu; nawawerenga monga mwa mawerengedwe ao ndi dzanja la mlembi Yeyeli, ndi kapitao Maseya, monga anawauza Hananiya kazembe wina wa mfumu.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:5-18