2 Mbiri 26:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anthu onse Ayuda anatenga Uziya, ndiye wa zaka khumi mphambu zisanu ndi cimodzi, namlonga ufumu m'malo mwa atate wace Amaziya.

2 Mbiri 26

2 Mbiri 26:1-3