2 Mbiri 25:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma sanapha ana ao, koma anacita monga umo mulembedwa m'cilamulo, m'buku la Mose, monga Yehova analamulira, ndi kuti, Atate asafere ana, ndi ana asafere atate; koma yense afere chimo lace lace.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:2-13