2 Mbiri 25:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Natenga golidi ndi siliva zonse, ndi zipangizo zonse zopezeka m'nyumba ya Mulungu kwa Obedi Edomu, ndi cuma ca nyumba ya mfumu, acikole omwe; nabwerera kumka ku Samariya.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:18-25