2 Mbiri 25:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Amaziya mfumu ya Yuda anafunsana ndi ompangira, natumiza kwa Yoasi mwana wa Yehoahazi mwana wa Yehu mfumu ya Israyeli, ndi kuti, Idzani, tionane maso.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:13-23