2 Mbiri 24:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ana a Ataliya mkazi woipa uja anathyola citseko ca nyumba ya Mulungu, natenga zopatulidwa zonse za nyumba ya Yehova kuzipereka kwa Baala.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:3-13