2 Mbiri 24:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Za ana ace tsono, ndi katundu wamkuru anamsenza, ndi kumanganso kwa nyumba ya Mulungu, taonani, zilembedwa m'buku lomasulira la mafumu. Ndipo Amaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:22-27