2 Mbiri 24:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atamcokera (popeza anamsiya wodwala nthenda zazikuru), anyamata ace anamcitira ciwembu, cifukwa ca mwazi wa ana a Yehoyada wansembe, namupha pakama pace, namwalira iye; ndipo anamuika m'mudzi wa Davide, koma osamuika m'manda a mafumu.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:16-27