2 Mbiri 24:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero mfumu Yoasi sanakumbukila zokoma anamcitirazi Yehoyada atate wace, koma anapha mwana wace; ndiye pomwalira anati, Yehova acipenye, nacifunse.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:15-27