2 Mbiri 24:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuika m'mudzi wa Davide, pakati pa mafumu; pakuti anacita zabwino m'Israyeli, ndi kwa Mulungu, ndi ku nyumba yace.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:9-23