2 Mbiri 24:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anacita ogwira nchito, nikula nchito mwa dzanja lao, nakhazikitsa iwo nyumba ya Mulungu monga mwa maonekedwe ace, nailimbitsa.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:11-22