2 Mbiri 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yoasi anali wa zaka zisanu ndi ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mace ndiye Zibiya wa ku Beereseba.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:1-3