2 Mbiri 23:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Alevi ndi Ayuda onse anacita monga mwa zonse anawauza Yehoyada wansembe; natenga yense amuna ace alowe dzuwa la Sabata pamodzi ndi oturuka dzuwa la Sabata; pakuti Yehoyada wansembe sanamasula zigawo.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:4-12