2 Mbiri 23:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo anayendayenda mwa Yuda, nasonkhanitsa Alevi m'midzi yonse ya Yuda, ndi akuru a nyumba za makolo m'Israyeli; nadza iwo ku Yerusalemu.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:1-8