2 Mbiri 22:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahaziya anali wa zaka makumi anai mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu caka cimodzi; ndi dzina la mace ndiye Ataliya mwana wa Omri.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:1-8