2 Mbiri 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Ataliya anaona kuti mwana wace adafa, anauka, naononga mbeu yonse yacifumu ya nyumba ya Yuda.

2 Mbiri 22

2 Mbiri 22:1-12