2 Mbiri 21:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo atate wao anawapatsa mphatso zazikuru, za siliva, ndi za golidi, ndi za mtengo wace, pamodzi ndi midzi yamalinga m'Yuda; koma ufumu anauninkha kwa Yehoramu; pakuti ndiye mwana wace woyamba.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:1-4