2 Mbiri 21:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndiwo anakwerera Yuda, nathyolamo, nalanda cuma conse cinapezeka m'nyumba ya mfumu, ndi ana ace omwe, ndi akazi ace, osamsiyira mwana, koma Yehoahazi yekha mwana wace wamng'ono.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:16-20