2 Mbiri 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehosafati anagona pamodzi ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; ndi Yehoramu mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:1-4