2 Mbiri 20:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nati, Yehova Mulungu wa makolo athu, Inu sindinu Mulungu wa m'Mwamba kodi? sindinu woweruza maufumu onse a amitundu kodi? ndi m'dzanja mwanu muli mphamvu yolimba; palibe wina wakulaka Inu.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:2-10