2 Mbiri 20:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Komatu misanje siinacotsedwa; popeza pamenepo anthu sadakonzere mitima yao kwa Mulungu wa makolo ao.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:30-37