2 Mbiri 20:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Yehosafati anakhala mfumu ya Yuda; anali wa zaka makumi atatu mphambu zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu zaka makumi awiri; ndi dzina la mace ndiye Azuba mwana wa Sili.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:27-36