2 Mbiri 20:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anadza anthu akuuza Yehosafati, kuti, Ukudzerani unyinji waukuru wa anthu ocokera tsidya la nyanja ku Aramu; ndipo taonani, ali ku Hazazoni Tamara, ndiwo Engedi.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:1-5