2 Mbiri 20:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Si kwanu kucita nkhondo kuno ai; cirimikani, imani, nimupenye cipulumutso ca Yehova pa inu Yuda ndi Yerusalemu; musaope, kapena kutenga nkhawa; mawa muwaturukire, popeza Yehova ali ndi inu.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:11-23