2 Mbiri 20:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mulungu wathu, simudzawaweruza? pakuti mwa ife mulibe mphamvu yakulimbana nao aunyinji ambiri awa akutidzera; ndipo sitidziwa ngati tidzatani, koma maso athu ali kwa Inu.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:9-17