2 Mbiri 20:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, taonani ana a Amoni, ndi Moabu, ndi a ku phiri la Seiri, amene simunalola Israyeli awalowere, pakuturuka iwo m'dziko la Aigupto, koma anawapambukira osawaononga;

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:5-16