2 Mbiri 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Munditumizirenso mitengo yamikungudza, ndi yamlombwa, ndi yambawa, ya ku Lebano; pakuti ndidziwa kuti anyamata anu adziwa kutema mitengo m'Lebano; ndipo taonani, anyamata anga adzakhala ndi anyamata anu,

2 Mbiri 2

2 Mbiri 2:1-16