2 Mbiri 2:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ali nayo mphamvu ndani yakummangira Iye nyumba, popeza thambo lam'mwambamwamba silimfikira? ndine yani ine tsono, kuti ndimmangire nyumba, koma kumfukizira cofukiza ndiko?

2 Mbiri 2

2 Mbiri 2:1-13