2 Mbiri 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Solomo anatumiza kwa Huramu mfumu ya Turo, ndi kuti, Monga momwe munacitira Davide atate wanga, ndi kumtumizira mikungudza yommangira nyumba yokhalamo, mundicitire ine momwemo.

2 Mbiri 2

2 Mbiri 2:1-6