2 Mbiri 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ife tidzatema mitengo ku Lebano monga mwa kusowa kwanu konse; ndipo tidzabwera nayo kwa inu yoyandamitsa paphaka kufikira ku Yopa; ndipo inu mudzakwera nayo ku Yerusalemu.

2 Mbiri 2

2 Mbiri 2:8-18