2 Mbiri 19:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturuka Yehu mwana wa Hanani mlauli kukomana naye, nati kwa mfumu Yehosafati, Muyenera kodi kuthandiza oipa, ndi kukonda amene adana ndi Yehova? Cifukwa ca ici ukugwerani mkwiyo wocokera kwa Yehova.

2 Mbiri 19

2 Mbiri 19:1-11