2 Mbiri 19:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, Amariya wansembe wamkuru, ndiye mkuru wanu m'mirandu yonse ya Yehova; ndi Zebadiya mwana wa Ismayeli, wolamulira nyumba ya Yuda, m'mirandu yonse ya mfumu; ndi Alevi akhale akapitao pamaso panu. Citani molimbika mtima, ndipo Yehova akhale ndi abwino.

2 Mbiri 19

2 Mbiri 19:5-11