2 Mbiri 18:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo mfumu ya Israyeli anamemeza aneneri amuna mazana anai, nanena nao, Kodi timuke kunkhondo ku Ramoti Gileadi kapena ndileke? Ndipo anati, Kweraniko, pakuti Mulungu adzaupereka m'dzanja la mfumu.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:1-8