2 Mbiri 18:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo munthu anaponya mubvi wace ciponyeponye, namlasa pakati pa maluma a maraya ace acitsulo. Potero anati kwa woyendetsa garetayo, Tembenuza dzanja lako, nundicotse ku khamu la nkhondo kuno, pakuti ndalasidwa.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:28-34