2 Mbiri 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nuti uwu, Ndidzaturuka ndi kukhala mzimu wonama m'kamwa mwa aneneri ace onse. Nati Iye, Udzamnyengadi, nudzakhoza; turuka, ukatero kumene.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:16-28