2 Mbiri 17:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace Yehova anakhazikitsa ufumuwo m'dzanja lace, ndi onse Ayuda anabwera nayo mitulo kwa Yehosafati; ndipo zidamcurukira cuma ndi ulemu.

2 Mbiri 17

2 Mbiri 17:2-15