2 Mbiri 17:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naika ankhondo m'midzi yonse yamalinga ya Yuda, naika aboma m'dziko la Yuda, ndi m'midzi ya Efraimu, imene adailanda Asa atate wace.

2 Mbiri 17

2 Mbiri 17:1-11