2 Mbiri 17:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi wotsatana naye Amasiya mwana wa Zikri, wodzipereka kwa Yehova mwaufulu, ndi pamodzi ndi iye ngwazi zamphamvu zikwi mazana awiri;

2 Mbiri 17

2 Mbiri 17:11-19