2 Mbiri 17:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kuopsa kwa Yehova kunagwera maufumu a maiko ozungulira Yuda; momwemo sanayambana ndi Yehosafati.

2 Mbiri 17

2 Mbiri 17:5-13