2 Mbiri 16:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Asa mfumu anatenga Ayuda onse, ndipo anatuta miyala ya ku Rama, ndi mitengo yace, imene Basa adamanga nayo, namangira Geba ndi Mizipa.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:4-7