2 Mbiri 16:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuika m'manda ace adadzisemerawo m'mudzi wa Davide, namgoneka pa kama wodzala ndi zonunkhira za mitundu mitundu, monga mwa makonzedwe a osanganiza; ndipo anampserezera zopsereza zambiri.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:9-14