2 Mbiri 15:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo analowa nazo zopatulika za atate wace, ndi zopatulika zace zace, ku nyumba ya Mulungu; ndizo siliva, ndi golidi, ndi zipangizo.

2 Mbiri 15

2 Mbiri 15:16-19