2 Mbiri 15:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi kuti yense wosafuna Yehova Mulungu wa Israyeli aphedwe, ngakhale wamng'ono kapena wamkuru, wamwamuna kapena wamkazi.

2 Mbiri 15

2 Mbiri 15:4-19