2 Mbiri 13:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anakhala mfumu m'Yerusalemu zaka zitatu; ndi dzina la mace ndiye Mikaya mwana wamkazi wa Uriyeli wa ku Gibeya. Ndipo panali nkhondo pakati pa Abiya ndi Yerobiamu.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:1-4