2 Mbiri 13:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo anacepetsedwa ana a Israyeli nthawi ija, nalakika ana a Yuda; popeza anatama Yehova Mulungu wa makolo ao.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:8-22